Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Atesalonika 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa Ambuye mwini adzatsika kumwamba,+ ndi mfuu yolamula ya mawu a mkulu wa angelo,+ ndi lipenga+ la Mulungu. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzauka choyamba.+

  • Aheberi 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+

  • Chivumbulutso 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba akuti: “Lemba: Odala ndiwo anthu amene akufa+ mwa Ambuye+ kuyambira pa nthawi ino kupita m’tsogolo.+ Mzimu ukuti, alekeni akapumule ku ntchito yawo imene anaigwira mwakhama, pakuti zimene anachita zikupita nawo limodzi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena