Mateyu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane. Maliko 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+ Yohane 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Petulo atatembenuka, anaona wophunzira amene Yesu anali kumukonda+ akuwalondola. Wophunzira ameneyu ndi amene pa chakudya chamadzulo chija anatsamira pachifuwa cha Yesu ndi kumufunsa kuti: “Ambuye, ndani amene akufuna kukuperekani?”
2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane.
19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+
20 Petulo atatembenuka, anaona wophunzira amene Yesu anali kumukonda+ akuwalondola. Wophunzira ameneyu ndi amene pa chakudya chamadzulo chija anatsamira pachifuwa cha Yesu ndi kumufunsa kuti: “Ambuye, ndani amene akufuna kukuperekani?”