Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti monga Atate amaukitsa akufa ndi kuwapatsa moyo,+ nayenso Mwana amapereka moyo kwa amene iye wafuna kuwapatsa.+ Yohane 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti chifuniro cha Atate wanga ndi chakuti, aliyense woona Mwana ndi kukhulupirira mwa iye akhale nawo moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa pa tsiku lomaliza.”+ Chivumbulutso 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Simuna lemba kuti: Izi ndi zimene akunena ‘Woyamba ndi Wotsiriza,’+ amene anafa n’kukhalanso ndi moyo.+
21 Pakuti monga Atate amaukitsa akufa ndi kuwapatsa moyo,+ nayenso Mwana amapereka moyo kwa amene iye wafuna kuwapatsa.+
40 Pakuti chifuniro cha Atate wanga ndi chakuti, aliyense woona Mwana ndi kukhulupirira mwa iye akhale nawo moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa pa tsiku lomaliza.”+
8 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Simuna lemba kuti: Izi ndi zimene akunena ‘Woyamba ndi Wotsiriza,’+ amene anafa n’kukhalanso ndi moyo.+