Mateyu 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma amene adzapirire+ mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke.+ Aheberi 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+ Aheberi 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza+ ngati amenewo a anthu ochimwa, amene mwa kulankhula koteroko anali kungodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope ndiponso kuti musalefuke.+
36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+
3 Ndithudi, ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza+ ngati amenewo a anthu ochimwa, amene mwa kulankhula koteroko anali kungodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope ndiponso kuti musalefuke.+