Mateyu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uthenga wabwino+ uwu wa ufumu+ udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni ku mitundu yonse,+ kenako mapeto+ adzafika. Maliko 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, m’mitundu yonse uthenga wabwino+ uyenera ulalikidwe choyamba.+
14 Uthenga wabwino+ uwu wa ufumu+ udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni ku mitundu yonse,+ kenako mapeto+ adzafika.