Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+