Chivumbulutso 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu yoyaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba.+ Inagwera pa gawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+
10 Tsopano mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu yoyaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba.+ Inagwera pa gawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+