2 Mbiri 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+ Zekariya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo, anthu adzalira kwambiri mu Yerusalemu ngati mmene analirira ku Hadadirimoni, m’chigwa cha Megido.+ Chivumbulutso 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndinaona chilombo,+ mafumu+ a dziko lapansi, ndi magulu awo ankhondo atasonkhana pamodzi kuti amenyane+ ndi wokwera pahatchi+ uja ndi gulu lake lankhondo.
22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+
11 Pa tsiku limenelo, anthu adzalira kwambiri mu Yerusalemu ngati mmene analirira ku Hadadirimoni, m’chigwa cha Megido.+
19 Ndipo ndinaona chilombo,+ mafumu+ a dziko lapansi, ndi magulu awo ankhondo atasonkhana pamodzi kuti amenyane+ ndi wokwera pahatchi+ uja ndi gulu lake lankhondo.