Chivumbulutso 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo kumwamba kunakanganuka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa m’malo awo.+
14 Ndipo kumwamba kunakanganuka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa m’malo awo.+