Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 38:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi unalowapo munkhokwe ya chipale chofewa,+

      Kapena umaziona nkhokwe za matalala,+

  • Yobu 38:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zimene ndazisungira nthawi ya zowawa,

      Ndi tsiku lomenyana komanso lankhondo?+

  • Yesaya 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu ndi wanyonga.+ Monga mvula yamabingu ndi yamatalala,+ mvula yamphepo yowononga, ndiponso monga mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,+ iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena