Mateyu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,) Yakobo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma nzeru+ yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+
15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)
17 Koma nzeru+ yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+