Yesaya 47:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+ khala pansi mwakachetechete+ ndipo ulowe mu mdima.+ Pakuti anthu sadzakutchulanso kuti Dona+ wa Maufumu.+ Chivumbulutso 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 limene mafumu a dziko lapansi anachita nalo dama,+ ndipo linaledzeretsa anthu okhala padziko lapansi ndi vinyo wa dama* lake.”+
5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+ khala pansi mwakachetechete+ ndipo ulowe mu mdima.+ Pakuti anthu sadzakutchulanso kuti Dona+ wa Maufumu.+
2 limene mafumu a dziko lapansi anachita nalo dama,+ ndipo linaledzeretsa anthu okhala padziko lapansi ndi vinyo wa dama* lake.”+