Yesaya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamapeto pa zaka 70, Yehova adzakumbukira Turo. Mzindawo udzayambiranso kulandira malipiro+ ndipo udzachita uhule ndi maufumu onse a padziko lapansi.+
17 Pamapeto pa zaka 70, Yehova adzakumbukira Turo. Mzindawo udzayambiranso kulandira malipiro+ ndipo udzachita uhule ndi maufumu onse a padziko lapansi.+