Yeremiya 50:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kugwidwa kwa Babulo,+ ndipo kulira kudzamveka pakati pa mitundu ya anthu.”+ Ezekieli 27:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu onse okhala m’zilumba+ adzakuyang’anitsitsa modabwa ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zonse zidzaoneka zankhawa.+
46 Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kugwidwa kwa Babulo,+ ndipo kulira kudzamveka pakati pa mitundu ya anthu.”+
35 Anthu onse okhala m’zilumba+ adzakuyang’anitsitsa modabwa ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zonse zidzaoneka zankhawa.+