Mateyu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+
6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+