Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+ Ezekieli 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndidzathetsa phokoso la kuimba kwako+ ndipo phokoso la azeze ako silidzamvekanso.+
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+