Maliko 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno tsiku loyenera+ linafika pamene Herode anakonzera chakudya chamadzulo nduna zake, akuluakulu a asilikali ndi atsogoleri a mu Galileya, pa tsiku lokumbukira kubadwa kwake.+
21 Ndiyeno tsiku loyenera+ linafika pamene Herode anakonzera chakudya chamadzulo nduna zake, akuluakulu a asilikali ndi atsogoleri a mu Galileya, pa tsiku lokumbukira kubadwa kwake.+