Yesaya 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zimenezi zidzakugwera ndithu,+ chifukwa cha zamatsenga zochuluka zimene wachita, chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zako zamatsenga, ndiponso chifukwa chakuti wazichita kwambiri.+ Agalatiya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko, Chivumbulutso 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo sanalape ntchito zawo zopha anthu,+ zamizimu,+ dama lawo, ngakhalenso umbava wawo.
9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zimenezi zidzakugwera ndithu,+ chifukwa cha zamatsenga zochuluka zimene wachita, chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zako zamatsenga, ndiponso chifukwa chakuti wazichita kwambiri.+
20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,