Salimo 117:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu mafuko onse.+