Yohane 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Wotumidwa ndi Mulungu amalankhula mawu a Mulungu,+ pakuti akafuna kupereka mzimu sachita kuyeza pamuyezo.+ Yohane 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Wochokera kwa Mulungu amamvetsera mawu a Mulungu.+ Ndiye chifukwa chake inu simumvetsera, chifukwa sindinu ochokera kwa Mulungu.”+
34 Wotumidwa ndi Mulungu amalankhula mawu a Mulungu,+ pakuti akafuna kupereka mzimu sachita kuyeza pamuyezo.+
47 Wochokera kwa Mulungu amamvetsera mawu a Mulungu.+ Ndiye chifukwa chake inu simumvetsera, chifukwa sindinu ochokera kwa Mulungu.”+