Chivumbulutso 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mngeloyo+ anatsitsira chikwakwa chake kudziko lapansi mwamphamvu, ndi kumweta mpesa+ wa padziko lapansi. Ndiyeno anauponya m’choponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+
19 Mngeloyo+ anatsitsira chikwakwa chake kudziko lapansi mwamphamvu, ndi kumweta mpesa+ wa padziko lapansi. Ndiyeno anauponya m’choponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+