Chivumbulutso 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+ Chivumbulutso 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,+ ooneka ngati achule,+ akutuluka m’kamwa mwa chinjoka,+ m’kamwa mwa chilombo,+ ndi m’kamwa mwa mneneri wonyenga.+
11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+
13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,+ ooneka ngati achule,+ akutuluka m’kamwa mwa chinjoka,+ m’kamwa mwa chilombo,+ ndi m’kamwa mwa mneneri wonyenga.+