Chivumbulutso 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chinachitanso zizindikiro zazikulu,+ moti chinapangitsa ngakhale moto kugwera padziko lapansi kuchokera kumwamba, anthu akuona.
13 Chinachitanso zizindikiro zazikulu,+ moti chinapangitsa ngakhale moto kugwera padziko lapansi kuchokera kumwamba, anthu akuona.