Chivumbulutso 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse,+ olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti apatsidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pamphumi pawo.+
16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse,+ olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti apatsidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pamphumi pawo.+