-
Genesis 39:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Potifara anasiya zinthu zake zonse mʼmanja mwa Yosefe, moti sankadera nkhawa chilichonse kupatulapo kusankha chakudya choti adye. Komanso Yosefe anali wooneka bwino ndiponso wa thupi loumbika bwino.
-