Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamene amalonda a Chimidiyani+ aja ankadutsa, abale a Yosefe anamutulutsa mʼchitsimemo nʼkumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo amalondawo anapita naye ku Iguputo.
28 Pamene amalonda a Chimidiyani+ aja ankadutsa, abale a Yosefe anamutulutsa mʼchitsimemo nʼkumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo amalondawo anapita naye ku Iguputo.