-
Genesis 47:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno Yosefe anauza anthuwo kuti: “Onani, ndakugulani inu lero limodzi ndi minda yanu kuti mukhale a Farao. Tengani mbewu iyi, mukadzale mʼmindamo.
-