Genesis 45:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo, ndipo ndi wolamulira wa dziko lonse la Iguputo!”+ Koma Yakobo atamva zimenezo sanawayankhe chifukwa sanawakhulupirire.+
26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo, ndipo ndi wolamulira wa dziko lonse la Iguputo!”+ Koma Yakobo atamva zimenezo sanawayankhe chifukwa sanawakhulupirire.+