-
Genesis 46:33, 34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Farao akakuitanani nʼkukufunsani kuti, ‘Kodi mumagwira ntchito yanji?’ 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni+ kuno, chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+
-