Genesis 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziko la Iguputo lili mʼmanja mwako, choncho uwapatse malo abwino kwambiri.+ Uwauze kuti akhale ku Goseni, ndipo ngati ukudziwapo amuna olimbikira ntchito, uwaike kuti akhale oyangʼanira ziweto zanga.”
6 Dziko la Iguputo lili mʼmanja mwako, choncho uwapatse malo abwino kwambiri.+ Uwauze kuti akhale ku Goseni, ndipo ngati ukudziwapo amuna olimbikira ntchito, uwaike kuti akhale oyangʼanira ziweto zanga.”