9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Ndili ndi zaka 130 ndipo pa zaka zimenezi ndakhala ndikuyendayenda mʼmalo osiyanasiyana. Ndakhala ndi moyo zaka zowerengeka komanso zosautsa,+ ndipo si zambiri poyerekezera ndi zaka zimene makolo anga akhala akuyendayenda mʼmalo osiyanasiyana.”+