Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wamva kudandaula kwanga kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Simiyoni.*+
33 Leya anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wamva kudandaula kwanga kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Simiyoni.*+