Genesis 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+
34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+