Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma makhalidwe a Ere, mwana woyamba wa Yuda, sanasangalatse Yehova ndipo Yehova anamupha.

  • Genesis 38:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma Onani anadziwa kuti anawo sadzakhala ake.+ Choncho, nthawi zonse akagona ndi mkazi wa mʼbale wakeyo, ankataya pansi umuna wake kuti asamuberekere ana mʼbale wakeyo.+ 10 Zimene ankachitazo zinali zoipa pamaso pa Yehova, choncho nayenso anamupha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena