1 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana woyamba wa Benjamini+ anali Bela,+ wachiwiri anali Asibeli,+ wachitatu anali Ahara, 1 Mbiri 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Bela anali Adara, Gera,+ Abihudi,