-
Genesis 35:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mulungu anamuuza kuti: “Dzina lako ndi Yakobo.+ Kuyambira lero, dzina lako silikhalanso Yakobo, koma likhala Isiraeli.” Choncho anayamba kumutchula kuti Isiraeli.+ 11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe,+ ndipo zina mwa mbadwa zako zidzakhala* mafumu.+
-