Genesis 43:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yuda anauza Isiraeli bambo ake kuti: “Ndiloleni ndimutenge mnyamatayu+ kuti tinyamuke tizipita kuti tikhalebe ndi moyo tisafe,+ inuyo ndi ife, limodzi ndi ana athuwa.+ Genesis 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe nʼkunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndikukupemphani. Ndiloleni kapolo wanune kuti ndinene mawu amodzi okha. Chonde musandipsere mtima, chifukwa inu muli ngati Farao yemwe.+
8 Kenako Yuda anauza Isiraeli bambo ake kuti: “Ndiloleni ndimutenge mnyamatayu+ kuti tinyamuke tizipita kuti tikhalebe ndi moyo tisafe,+ inuyo ndi ife, limodzi ndi ana athuwa.+
18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe nʼkunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndikukupemphani. Ndiloleni kapolo wanune kuti ndinene mawu amodzi okha. Chonde musandipsere mtima, chifukwa inu muli ngati Farao yemwe.+