-
Genesis 41:39, 40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi, palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe. 40 Iweyo ukhala woyangʼanira nyumba yanga, ndipo anthu anga onse azimvera chilichonse chimene iweyo ungawauze.+ Koma ine ndekha ndikhala wamkulu kwa iwe chifukwa ndine mfumu.”
-