2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova* sakuchedwa kukwaniritsa zimene analonjeza+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa. Koma akukulezerani mtima chifukwa sakufuna kuti munthu aliyense adzawonongedwe, koma akufuna kuti anthu onse alape.+
9 Yehova* sakuchedwa kukwaniritsa zimene analonjeza+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa. Koma akukulezerani mtima chifukwa sakufuna kuti munthu aliyense adzawonongedwe, koma akufuna kuti anthu onse alape.+