-
Genesis 46:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza mʼdziko la Kanani. Kenako Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.
-