Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno Yehova anayamba kumva fungo losangalatsa.* Choncho Yehova ananena mumtima mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo a anthu amakhala oipa kuyambira ali ana.+ Ndipo sindidzaphanso chamoyo chilichonse ngati mmene ndachitiramu.+

  • Yeremiya 17:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mtima ndi wopusitsa* kwambiri kuposa chinthu chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+

      Ndi ndani angaudziwe?

  • Mateyu 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mwachitsanzo, mumtima mumachokera maganizo oipa awa:+ maganizo a kupha anthu, a chigololo, a chiwerewere,* a kuba, maumboni onama komanso kunyoza Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena