-
Genesis 14:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako mafumu a Sodomu ndi Gomora anayamba kuthawa. Koma chigwa cha Sidimu chinali ndi maenje aphula ambirimbiri, choncho iwo pothawa ankagwera mʼmaenje amenewo. Amene anatsala anathawira kudera lamapiri.
-