-
Genesis 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho zamoyo zamtundu uliwonse, zazimuna ndi zazikazi, zinalowa mʼchingalawamo mogwirizana ndi mmene Mulungu analamulira Nowa. Kenako Yehova anatseka chitseko.
-