Genesis 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mʼchaka cha 601 cha Nowa,+ mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, madzi anali ataphwa padziko lapansi. Nowa anatsegula chibowo chimene chinali padenga la chingalawacho nʼkuyangʼana kunja ndipo anaona kuti nthaka yayamba kuuma.
13 Tsopano mʼchaka cha 601 cha Nowa,+ mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, madzi anali ataphwa padziko lapansi. Nowa anatsegula chibowo chimene chinali padenga la chingalawacho nʼkuyangʼana kunja ndipo anaona kuti nthaka yayamba kuuma.