Genesis 20:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndinachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu akuno saopa Mulungu, andipha chifukwa cha mkazi wangayu.’+ 12 Komabe, ndi mchemwali wangadi ameneyu. Bambo athu ndi amodzi, tinangosiyana mayi, ndipo ndinamukwatira.+
11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndinachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu akuno saopa Mulungu, andipha chifukwa cha mkazi wangayu.’+ 12 Komabe, ndi mchemwali wangadi ameneyu. Bambo athu ndi amodzi, tinangosiyana mayi, ndipo ndinamukwatira.+