-
Genesis 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndiyeno Abimeleki anatenga nkhosa, ngʼombe ndiponso antchito aamuna ndi aakazi nʼkumupatsa Abulahamu. Anamubwezeranso Sara mkazi wake.
-