Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+ Salimo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munamupatsa mphamvu kuti alamulire ntchito za manja anu.+Mwaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake:
4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+