Genesis 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake Abulamu anasamutsa tenti yake kumeneko. Kuyambira pa nthawi imeneyi, iye ankangokhalira kumanga ndi kusamutsa msasa, kulowera ku Negebu.+ Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ nʼkupita kudziko la Negebu ndipo anayamba kukhala pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+ Pamene ankakhala* ku Gerari,+
9 Pambuyo pake Abulamu anasamutsa tenti yake kumeneko. Kuyambira pa nthawi imeneyi, iye ankangokhalira kumanga ndi kusamutsa msasa, kulowera ku Negebu.+
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ nʼkupita kudziko la Negebu ndipo anayamba kukhala pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+ Pamene ankakhala* ku Gerari,+