Genesis 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mbiri ya Tera ndi iyi. Tera anabereka Abulamu, Nahori ndi Harana. Harana anabereka Loti.+