Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapereka chakudya kwa zinyama,+Amapatsa ana a makwangwala chakudya chimene akulirira.+ Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?
26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?